-
Hagai 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndinalamula kuti chilala chigwe padziko lapansi, pamapiri, pambewu, pavinyo watsopano, pamafuta, pazomera zonse, pa anthu, paziweto ndiponso pantchito iliyonse ya manja anu.’”
-