Hagai 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Hagai, amene anatumidwa ndi Yehova, analankhula ndi anthuwo mogwirizana ndi ntchito imene Yehova anamʼpatsa. Iye anati: “‘Ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova.”
13 Hagai, amene anatumidwa ndi Yehova, analankhula ndi anthuwo mogwirizana ndi ntchito imene Yehova anamʼpatsa. Iye anati: “‘Ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova.”