Hagai 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Kodi pakati panu pali aliyense amene anaona ulemerero umene nyumbayi* inali nawo poyamba?+ Kodi panopa mukuiona bwanji? Kodi simukuona kuti ilibiretu ulemerero tikayerekeza ndi poyamba?’+
3 ‘Kodi pakati panu pali aliyense amene anaona ulemerero umene nyumbayi* inali nawo poyamba?+ Kodi panopa mukuiona bwanji? Kodi simukuona kuti ilibiretu ulemerero tikayerekeza ndi poyamba?’+