Hagai 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Kumbukirani zimene ndinakulonjezani pamene munkatuluka mʼdziko la Iguputo.+ Panopa mzimu wanga udakali ndi inu.*+ Choncho musachite mantha.’”+ Hagai Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,4/15/2006, tsa. 24
5 ‘Kumbukirani zimene ndinakulonjezani pamene munkatuluka mʼdziko la Iguputo.+ Panopa mzimu wanga udakali ndi inu.*+ Choncho musachite mantha.’”+