Hagai 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndinakulangani ndipo ndinawononga ntchito za manja anu pobweretsa mphepo yotentha, matenda a mbewu a chuku+ ndi matalala, koma palibe aliyense amene anabwerera kwa ine,’ watero Yehova.
17 Ine ndinakulangani ndipo ndinawononga ntchito za manja anu pobweretsa mphepo yotentha, matenda a mbewu a chuku+ ndi matalala, koma palibe aliyense amene anabwerera kwa ine,’ watero Yehova.