Zekariya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “‘Musakhale ngati makolo anu amene aneneri akale anawauza kuti: “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Chonde, siyani njira zanu zoipa ndiponso zochita zanu zoipa.’”’+ ‘Koma iwo sanamvere ndipo sanatsatire mawu anga,’+ watero Yehova.
4 “‘Musakhale ngati makolo anu amene aneneri akale anawauza kuti: “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Chonde, siyani njira zanu zoipa ndiponso zochita zanu zoipa.’”’+ ‘Koma iwo sanamvere ndipo sanatsatire mawu anga,’+ watero Yehova.