Zekariya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno iwo anauza mngelo wa Yehova amene anaima pakati pa mitengo ya mchisu uja kuti: “Ife tayendayenda padziko lonse lapansi ndipo taona kuti pali bata komanso palibe chosokoneza.”+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 30
11 Ndiyeno iwo anauza mngelo wa Yehova amene anaima pakati pa mitengo ya mchisu uja kuti: “Ife tayendayenda padziko lonse lapansi ndipo taona kuti pali bata komanso palibe chosokoneza.”+