Zekariya 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho mngelo wa Yehova anati: “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, kodi Yerusalemu ndiponso mizinda ya Yuda+ imene munaikwiyira kwa zaka 70 zimenezi,+ simuichitira chifundo mpaka liti?” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:12 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 30
12 Choncho mngelo wa Yehova anati: “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, kodi Yerusalemu ndiponso mizinda ya Yuda+ imene munaikwiyira kwa zaka 70 zimenezi,+ simuichitira chifundo mpaka liti?”