Zekariya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mngeloyo anauza mnzakeyo kuti: “Thamanga ukauze mnyamata uyo kuti, ‘“Mu Yerusalemu anthu azidzakhalamo+ ngati mzinda wopanda mpanda chifukwa cha anthu onse ndiponso ziweto zimene zili mmenemo.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 31
4 Mngeloyo anauza mnzakeyo kuti: “Thamanga ukauze mnyamata uyo kuti, ‘“Mu Yerusalemu anthu azidzakhalamo+ ngati mzinda wopanda mpanda chifukwa cha anthu onse ndiponso ziweto zimene zili mmenemo.+