Zekariya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Bwerani! Bwerani! Thawani mʼdziko lakumpoto,”+ watero Yehova. “Chifukwa ndinakubalalitsirani kumbali zonse za dziko lapansi,”+ watero Yehova.
6 “Bwerani! Bwerani! Thawani mʼdziko lakumpoto,”+ watero Yehova. “Chifukwa ndinakubalalitsirani kumbali zonse za dziko lapansi,”+ watero Yehova.