Zekariya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Fuula chifukwa cha chisangalalo, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,*+ popeza ine ndikubwera+ ndipo ndidzakhala pakati pako,”+ watero Yehova.
10 Fuula chifukwa cha chisangalalo, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,*+ popeza ine ndikubwera+ ndipo ndidzakhala pakati pako,”+ watero Yehova.