Zekariya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pa tsiku limenelo mitundu yambiri ya anthu idzakhala kumbali ya Yehova+ ndipo adzakhala anthu anga. Ine ndidzakhala pakati pako.” Ndipo udzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa iwe. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, ptsa. 27-28 Tsiku la Yehova, ptsa. 144-145, 175-176
11 “Pa tsiku limenelo mitundu yambiri ya anthu idzakhala kumbali ya Yehova+ ndipo adzakhala anthu anga. Ine ndidzakhala pakati pako.” Ndipo udzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa iwe.