-
Zekariya 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Anthu nonsenu, khalani chete pamaso pa Yehova, chifukwa iye wanyamuka pamalo ake oyera okhala ndipo akufuna kuchitapo kanthu.
-