Zekariya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mulungu anandionetsa Yoswa+ mkulu wa ansembe, ataimirira pamaso pa mngelo wa Yehova. Satana+ anali ataima kudzanja lamanja la Yoswa kuti azimutsutsa. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 11
3 Ndiyeno Mulungu anandionetsa Yoswa+ mkulu wa ansembe, ataimirira pamaso pa mngelo wa Yehova. Satana+ anali ataima kudzanja lamanja la Yoswa kuti azimutsutsa.