Zekariya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mngelo wa Yehovayo anauza Satana kuti: “Iwe Satana, Yehova akudzudzule!+ Yehova amene wasankha Yerusalemu+ akudzudzule. Kodi munthu uyu sali ngati chikuni chimene chapulumutsidwa pamoto kuti chisapse?” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 11
2 Kenako mngelo wa Yehovayo anauza Satana kuti: “Iwe Satana, Yehova akudzudzule!+ Yehova amene wasankha Yerusalemu+ akudzudzule. Kodi munthu uyu sali ngati chikuni chimene chapulumutsidwa pamoto kuti chisapse?”