Zekariya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mngeloyo anauza anthu amene anaima patsogolo pake kuti: “Muvuleni zovala zonyansazo.” Kenako anauza Yoswa kuti: “Waona, ndakuchotsera zolakwa zako ndipo uvekedwa zovala zabwino kwambiri.”*+
4 Mngeloyo anauza anthu amene anaima patsogolo pake kuti: “Muvuleni zovala zonyansazo.” Kenako anauza Yoswa kuti: “Waona, ndakuchotsera zolakwa zako ndipo uvekedwa zovala zabwino kwambiri.”*+