Zekariya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ndinanena kuti: “Auzeni kuti amuveke nduwira yoyera kumutu kwake.”+ Ndipo anamuvekadi nduwira yoyera kumutu kwake komanso zovala zina. Apa nʼkuti mngelo wa Yehova ataima chapafupi.
5 Choncho ndinanena kuti: “Auzeni kuti amuveke nduwira yoyera kumutu kwake.”+ Ndipo anamuvekadi nduwira yoyera kumutu kwake komanso zovala zina. Apa nʼkuti mngelo wa Yehova ataima chapafupi.