Zekariya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ‘Tamvetsera iwe Yoswa mkulu wa ansembe ndi anzako amene akhala pansi kutsogolo kwako, chifukwa amuna amenewa ali ngati chizindikiro. Ine ndibweretsa mtumiki wanga+ dzina lake Mphukira.+
8 ‘Tamvetsera iwe Yoswa mkulu wa ansembe ndi anzako amene akhala pansi kutsogolo kwako, chifukwa amuna amenewa ali ngati chizindikiro. Ine ndibweretsa mtumiki wanga+ dzina lake Mphukira.+