Zekariya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taonani mwala umene ndauika pamaso pa Yoswa. Mwala umenewu uli ndi maso 7 ndipo pamwalawu ndilembapo zinthu mochita kugoba. Ndidzachotsa zolakwa za dzikoli tsiku limodzi,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
9 Taonani mwala umene ndauika pamaso pa Yoswa. Mwala umenewu uli ndi maso 7 ndipo pamwalawu ndilembapo zinthu mochita kugoba. Ndidzachotsa zolakwa za dzikoli tsiku limodzi,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.