Zekariya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Pa tsiku limenelo aliyense adzaitana mnzake kuti abwere pansi pa mtengo wake wa mpesa ndiponso wa mkuyu,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”
10 ‘Pa tsiku limenelo aliyense adzaitana mnzake kuti abwere pansi pa mtengo wake wa mpesa ndiponso wa mkuyu,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”