2 Kenako anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani?”
Ndinayankha kuti: “Ndikuona choikapo nyale chagolide yekhayekha.+ Pamwamba pake pali mbale yolowa. Choikapo nyalecho chili ndi nyale 7,+ inde nyale 7, ndipo nyale zimene zili pachoikapo nyalecho, zilinso ndi mapaipi 7.