Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2022, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,4/15/2006, tsa. 23
6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.