Zekariya 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale Zerubabele+ atakumana ndi chopinga chachikulu ngati phiri, chidzasalazidwa nʼkukhala malo afulati.+ Iye adzabweretsa mwala wotsiriza ndipo anthu adzafuula kuti: “Koma mwalawu ndiye ndi wokongola bwanji! Koma ndiye ndi wokongola!”’” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:7 Nsanja ya Olonda,4/15/2006, ptsa. 23-24, 25-26
7 Ngakhale Zerubabele+ atakumana ndi chopinga chachikulu ngati phiri, chidzasalazidwa nʼkukhala malo afulati.+ Iye adzabweretsa mwala wotsiriza ndipo anthu adzafuula kuti: “Koma mwalawu ndiye ndi wokongola bwanji! Koma ndiye ndi wokongola!”’”