Zekariya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinafunsa mngelo uja kuti: “Kodi mitengo iwiri ya maolivi, imene wina uli kumanja ndipo wina kumanzere kwa choikapo nyalechi, ikuimira chiyani?”+
11 Ndiyeno ndinafunsa mngelo uja kuti: “Kodi mitengo iwiri ya maolivi, imene wina uli kumanja ndipo wina kumanzere kwa choikapo nyalechi, ikuimira chiyani?”+