Zekariya 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinamufunsanso kuti: “Kodi nthambi* ziwiri za mitengo ya maolivi, zimene zikuthira mafuta agolide mʼmbale yolowa kudzera mʼmapaipi awiri agolide, zikuimira chiyani?”
12 Ndinamufunsanso kuti: “Kodi nthambi* ziwiri za mitengo ya maolivi, zimene zikuthira mafuta agolide mʼmbale yolowa kudzera mʼmapaipi awiri agolide, zikuimira chiyani?”