Zekariya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako nditayangʼananso kumwamba ndinaona magaleta 4 akubwera kuchokera pakati pa mapiri awiri. Mapiriwo anali akopa.* Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, ptsa. 27-28 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 30
6 Kenako nditayangʼananso kumwamba ndinaona magaleta 4 akubwera kuchokera pakati pa mapiri awiri. Mapiriwo anali akopa.*