Zekariya 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mngeloyo anandiyankha kuti: “Magaletawa akuimira zolengedwa zauzimu 4+ zakumwamba zomwe zinakaima pamaso pa Ambuye wa dziko lonse lapansi+ ndipo zikubwera. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 28
5 Mngeloyo anandiyankha kuti: “Magaletawa akuimira zolengedwa zauzimu 4+ zakumwamba zomwe zinakaima pamaso pa Ambuye wa dziko lonse lapansi+ ndipo zikubwera.