-
Zekariya 6:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Anthu amene ali kutali adzabwera kudzamanga nawo kachisi wa Yehova.” Anthu inu mukadzamvera mawu a Yehova Mulungu wanu, mudzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa inu.’”
-