Zekariya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Muziweruza mwachilungamo chenicheni+ komanso muzisonyezana chikondi chokhulupirika+ ndi chifundo.
9 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Muziweruza mwachilungamo chenicheni+ komanso muzisonyezana chikondi chokhulupirika+ ndi chifundo.