Zekariya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye, mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosauka.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:10 Tsiku la Yehova, ptsa. 113-114
10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye, mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosauka.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+