14 ‘Ndipo ndinawabalalitsira ku mitundu yonse ya anthu imene sankaidziwa+ ngati atengedwa ndi mphepo yamkuntho. Dzikoli analisiya ndipo linakhala bwinja, popanda munthu wodutsamo kapena kubwereramo.+ Chifukwa anasandutsa dziko losiririka kukhala chinthu chochititsa mantha.’”