Zekariya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uthenga wokhudza dziko la Hadiraki: “Uwu ndi uthenga wa Yehova wokhudza dziko la Hadiraki,Ndipo makamaka ukupita kumzinda wa Damasiko.+Chifukwa maso a Yehova ali pa anthu,+Komanso pa mafuko onse a Isiraeli.
9 Uthenga wokhudza dziko la Hadiraki: “Uwu ndi uthenga wa Yehova wokhudza dziko la Hadiraki,Ndipo makamaka ukupita kumzinda wa Damasiko.+Chifukwa maso a Yehova ali pa anthu,+Komanso pa mafuko onse a Isiraeli.