Zekariya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Turo anamanga malo okwera omenyerapo nkhondo. Anadziunjikira siliva wambiri ngati fumbi,Ndiponso golide wambiri ngati dothi lamʼmisewu.+
3 Turo anamanga malo okwera omenyerapo nkhondo. Anadziunjikira siliva wambiri ngati fumbi,Ndiponso golide wambiri ngati dothi lamʼmisewu.+