Zekariya 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Asikeloni adzaona zimenezi ndipo adzachita mantha.Gaza adzamva ululu waukulu.Izi zidzachitikiranso Ekironi chifukwa amene ankamudalira wachititsidwa manyazi. Ku Gaza sikudzakhalanso mfumu,Ndipo ku Asikeloni sikudzakhalanso anthu.+
5 Asikeloni adzaona zimenezi ndipo adzachita mantha.Gaza adzamva ululu waukulu.Izi zidzachitikiranso Ekironi chifukwa amene ankamudalira wachititsidwa manyazi. Ku Gaza sikudzakhalanso mfumu,Ndipo ku Asikeloni sikudzakhalanso anthu.+