Zekariya 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzachotsa zinthu zamagazi mʼkamwa mwawo,Komanso chakudya chonyansa pakati pa mano awo.Ndipo aliyense amene adzatsale, adzakhala wa Mulungu wathu.Iye adzakhala ngati mtsogoleri mu Yuda,+Ndipo Ekironi adzakhala ngati munthu wa Chiyebusi.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Nsanja ya Olonda,5/15/1997, tsa. 197/1/1995, ptsa. 22-23
7 Ndidzachotsa zinthu zamagazi mʼkamwa mwawo,Komanso chakudya chonyansa pakati pa mano awo.Ndipo aliyense amene adzatsale, adzakhala wa Mulungu wathu.Iye adzakhala ngati mtsogoleri mu Yuda,+Ndipo Ekironi adzakhala ngati munthu wa Chiyebusi.+