Zekariya 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzamanga msasa kunja kwa nyumba yanga kuti ndizidzailondera,+Moti sipadzakhala munthu wolowa kapena kutuluka.Aliyense amene ankawagwiritsa ntchito* sadzadutsanso pakati pawo+Chifukwa ine ndaona ndi maso anga.*
8 Ndidzamanga msasa kunja kwa nyumba yanga kuti ndizidzailondera,+Moti sipadzakhala munthu wolowa kapena kutuluka.Aliyense amene ankawagwiritsa ntchito* sadzadutsanso pakati pawo+Chifukwa ine ndaona ndi maso anga.*