-
Zekariya 9:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndidzapinda Yuda kuti akhale uta wanga.
Efuraimu ndidzamuika pa uta umenewo ngati muvi.
Ndidzadzutsa ana ako, iwe Ziyoni,
Kuti aukire ana a Girisi.
Ndipo ndidzakusandutsa lupanga la msilikali.’
-