Zekariya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku limenelo, Yehova Mulungu adzapulumutsa nkhosa zake,Zomwe ndi anthu ake.+Popeza iwo adzakhala ngati miyala yamtengo wapatali yapachisoti chachifumu yomwe ikunyezimira mʼdziko lake.+
16 Pa tsiku limenelo, Yehova Mulungu adzapulumutsa nkhosa zake,Zomwe ndi anthu ake.+Popeza iwo adzakhala ngati miyala yamtengo wapatali yapachisoti chachifumu yomwe ikunyezimira mʼdziko lake.+