-
Zekariya 10:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Amafotokoza maloto opanda pake,
Ndipo saphula kanthu polimbikitsa anthu.
Nʼchifukwa chake adzasochere ngati nkhosa.
Iwo adzavutika chifukwa adzakhala opanda mʼbusa.
-