Zekariya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lira mofuula, iwe mtengo wa junipa,* chifukwa mtengo wa mkungudza wagwa.Mitengo ikuluikulu yawonongedwa. Lirani mofuula, inu mitengo ya thundu* ya ku Basana,Chifukwa nkhalango yowirira kwambiri ija yawonongedwa. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:2 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, tsa. 17
2 Lira mofuula, iwe mtengo wa junipa,* chifukwa mtengo wa mkungudza wagwa.Mitengo ikuluikulu yawonongedwa. Lirani mofuula, inu mitengo ya thundu* ya ku Basana,Chifukwa nkhalango yowirira kwambiri ija yawonongedwa.