-
Zekariya 11:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Tamverani! Abusa akulira mofuula,
Chifukwa ulemerero wawo watha.
Tamverani! Mikango yamphamvu ikubangula,
Chifukwa nkhalango zowirira za mʼmbali mwa mtsinje wa Yorodano zawonongedwa.
-