Zekariya 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene anazigula amazipha,+ koma saimbidwa mlandu. Amene akuzigulitsa+ akunena kuti: “Yehova atamandike chifukwa ndilemera.” Ndipo abusa ake sazichitira chifundo.’+
5 Amene anazigula amazipha,+ koma saimbidwa mlandu. Amene akuzigulitsa+ akunena kuti: “Yehova atamandike chifukwa ndilemera.” Ndipo abusa ake sazichitira chifundo.’+