-
Zekariya 11:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 ‘Sindidzachitiranso chifundo anthu okhala mʼdzikoli,’ watero Yehova. ‘Choncho ine ndidzachititsa kuti aliyense aziponderezedwa ndi mnzake ndiponso mfumu yake. Iwo adzawononga dzikoli, ndipo ine sindidzawapulumutsa mʼmanja mwawo.’”
-