-
Zekariya 11:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndipo ndinanena kuti: “Sindikuwetaninso. Amene akufa afe ndipo amene akuwonongeka, awonongeke. Otsalawo adyane.”
-