Zekariya 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Kaziponye mosungiramo chuma. Zimenezi ndi ndalama zochepa zimene aona kuti angandilipire.”+ Choncho ndinatenga ndalama 30 zasilivazo nʼkukaziponya mosungiramo chuma panyumba ya Yehova.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:13 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 15 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 13
13 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Kaziponye mosungiramo chuma. Zimenezi ndi ndalama zochepa zimene aona kuti angandilipire.”+ Choncho ndinatenga ndalama 30 zasilivazo nʼkukaziponya mosungiramo chuma panyumba ya Yehova.+
11:13 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 15 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 13