Zekariya 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsoka kwa mʼbusa wanga wopanda pake+ amene akusiya nkhosa.+ Lupanga lidzamutema padzanja ndi diso lake lakumanja. Dzanja lake lidzalumala kwambiri,Ndipo diso lake lamanja lidzachita khungu.”*
17 Tsoka kwa mʼbusa wanga wopanda pake+ amene akusiya nkhosa.+ Lupanga lidzamutema padzanja ndi diso lake lakumanja. Dzanja lake lidzalumala kwambiri,Ndipo diso lake lamanja lidzachita khungu.”*