Zekariya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uthenga wokhudza Isiraeli: “Awa ndi mawu a Yehova okhudza Isiraeli.”Yehova, amene anatambasula kumwamba,+Amene anayala maziko a dziko lapansi,+Komanso amene anapanga mzimu* umene uli mwa munthu, wanena kuti:
12 Uthenga wokhudza Isiraeli: “Awa ndi mawu a Yehova okhudza Isiraeli.”Yehova, amene anatambasula kumwamba,+Amene anayala maziko a dziko lapansi,+Komanso amene anapanga mzimu* umene uli mwa munthu, wanena kuti: