Zekariya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yerusalemu ndimusandutsa kapu imene imachititsa anthu a mitundu yonse yomuzungulira kuyenda dzandidzandi. Ndipo mdani adzazungulira Yuda komanso Yerusalemu.+
2 “Yerusalemu ndimusandutsa kapu imene imachititsa anthu a mitundu yonse yomuzungulira kuyenda dzandidzandi. Ndipo mdani adzazungulira Yuda komanso Yerusalemu.+