Zekariya 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa tsiku limenelo, Yerusalemu ndidzamusandutsa mwala wolemera* kwa anthu a mitundu yonse. Onse onyamula mwala umenewo, adzavulala koopsa.+ Anthu a mitundu yonse yapadziko lapansi adzasonkhana kuti amuukire.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:3 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, ptsa. 22-23
3 Pa tsiku limenelo, Yerusalemu ndidzamusandutsa mwala wolemera* kwa anthu a mitundu yonse. Onse onyamula mwala umenewo, adzavulala koopsa.+ Anthu a mitundu yonse yapadziko lapansi adzasonkhana kuti amuukire.+