Zekariya 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova adzayamba nʼkupulumutsa matenti a Yuda. Adzachita zimenezi kuti kukongola* kwa nyumba ya Davide ndi kukongola* kwa anthu a ku Yerusalemu, kusakhale kwakukulu kwambiri kuposa kwa Yuda. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:7 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 25
7 Yehova adzayamba nʼkupulumutsa matenti a Yuda. Adzachita zimenezi kuti kukongola* kwa nyumba ya Davide ndi kukongola* kwa anthu a ku Yerusalemu, kusakhale kwakukulu kwambiri kuposa kwa Yuda.